Yobu 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Dziwani kuti Mulungu mwiniwakeyo ndi amene wandisocheretsa,Ndipo wandizunguliza ndi ukonde wake wosakira nyama.+ Hoseya 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Kulikonse kumene iwo angapite, ndidzawatchera ndi ukonde.+ Ndidzawagwira ngati zolengedwa zouluka m’mlengalenga.+ Ndidzawalanga mogwirizana ndi chenjezo limene ndinauza msonkhano wawo.+
6 Dziwani kuti Mulungu mwiniwakeyo ndi amene wandisocheretsa,Ndipo wandizunguliza ndi ukonde wake wosakira nyama.+
12 “Kulikonse kumene iwo angapite, ndidzawatchera ndi ukonde.+ Ndidzawagwira ngati zolengedwa zouluka m’mlengalenga.+ Ndidzawalanga mogwirizana ndi chenjezo limene ndinauza msonkhano wawo.+