Salimo 66:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwatilowetsa mu ukonde wosakira nyama,+Mwatinyamulitsa katundu wolemera m’chiuno mwathu. Maliro 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye watumiza moto m’mafupa+ mwanga kuchokera kumwamba, ndipo wafooketsa fupa lililonse.Watchera ukonde+ kuti ukole mapazi anga. Wandibweza kumbuyo.Wandisandutsa mkazi wosiyidwa popanda thandizo. Ndikudwala tsiku lonse.+
13 Iye watumiza moto m’mafupa+ mwanga kuchokera kumwamba, ndipo wafooketsa fupa lililonse.Watchera ukonde+ kuti ukole mapazi anga. Wandibweza kumbuyo.Wandisandutsa mkazi wosiyidwa popanda thandizo. Ndikudwala tsiku lonse.+