8 “Pa nthawi imeneyo tinalanda dziko m’manja mwa mafumu awiri amenewo a Aamori+ amene anali kukhala m’dera la Yorodano, kuyambira m’chigwa* cha Arinoni+ mpaka kuphiri la Herimoni.+
10 Tinalanda mizinda yonse ya kudera lokwererapo, m’Giliyadi monse, m’Basana monse, mpaka ku Saleka+ ndi ku Edirei,+ mizinda ya m’dera la ufumu wa Ogi ku Basana.