Salimo 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+ Salimo 68:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 N’chifukwa chiyani inu mapiri a nsonga zitalizitali mumayang’ana mwanjiruPhiri limene Mulungu wafuna kukhalamo?+Yehova adzakhala m’phiri limenelo mpaka muyaya.+ Salimo 132:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wasankha Ziyoni,+Ndipo amafunitsitsa kuti akhale malo ake okhalamo. Iye amati:+
2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+
16 N’chifukwa chiyani inu mapiri a nsonga zitalizitali mumayang’ana mwanjiruPhiri limene Mulungu wafuna kukhalamo?+Yehova adzakhala m’phiri limenelo mpaka muyaya.+