1 Mbiri 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tsopano Davide anauza atsogoleri a Alevi kuti aike m’malo awo abale awo oimba+ okhala ndi zipangizo zoimbira.+ Zipangizozo zinali zoimbira za zingwe,+ azeze,+ ndi zinganga.+ Anawauza kuti aimbe mokweza kuti nyimbo zachisangalalo zimveke. Salimo 87:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kudzakhalanso oimba komanso ovina gule wovina mozungulira amene adzati:+“Akasupe anga onse ali mwa iwe.”+ Salimo 150:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mutamandeni mwa kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa.+Mutamandeni ndi choimbira cha zingwe ndi zeze.+
16 Tsopano Davide anauza atsogoleri a Alevi kuti aike m’malo awo abale awo oimba+ okhala ndi zipangizo zoimbira.+ Zipangizozo zinali zoimbira za zingwe,+ azeze,+ ndi zinganga.+ Anawauza kuti aimbe mokweza kuti nyimbo zachisangalalo zimveke.
7 Kudzakhalanso oimba komanso ovina gule wovina mozungulira amene adzati:+“Akasupe anga onse ali mwa iwe.”+
3 Mutamandeni mwa kuliza lipenga la nyanga ya nkhosa.+Mutamandeni ndi choimbira cha zingwe ndi zeze.+