Zefaniya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Anthu amene akundichonderera, anthu anga obalalitsidwa, adzandibweretsera mphatso kuchokera kuchigawo cha mitsinje ya ku Itiyopiya.+ Machitidwe 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho, ananyamuka ndi kupita. Kumeneko anakumana ndi nduna+ ya ku Itiyopiya,+ munthu waulamuliro pansi pa Kandake, mfumukazi ya Itiyopiya. Iye anali woyang’anira chuma chonse cha mfumukaziyo. Iyeyu anapita ku Yerusalemu kukapembedza Mulungu,+
10 “Anthu amene akundichonderera, anthu anga obalalitsidwa, adzandibweretsera mphatso kuchokera kuchigawo cha mitsinje ya ku Itiyopiya.+
27 Choncho, ananyamuka ndi kupita. Kumeneko anakumana ndi nduna+ ya ku Itiyopiya,+ munthu waulamuliro pansi pa Kandake, mfumukazi ya Itiyopiya. Iye anali woyang’anira chuma chonse cha mfumukaziyo. Iyeyu anapita ku Yerusalemu kukapembedza Mulungu,+