-
Salimo 144:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Tambasulani manja anu kuchokera kumwamba.+
Ndimasuleni ndi kundilanditsa m’madzi ambiri.+
Mundilanditse m’manja mwa anthu achilendo,+
-