Nehemiya 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo mbewu ya Isiraeli inadzipatula+ kwa anthu onse osakhala Aisiraeli.+ Atatero anaimirira ndi kuulula+ machimo awo+ ndi zolakwa za makolo awo.+ Salimo 54:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti pali anthu achilendo amene andiukira,Ndipo pali olamulira ankhanza amene akufuna moyo wanga.+Sanaike Mulungu patsogolo pawo.+ [Seʹlah.]
2 Pamenepo mbewu ya Isiraeli inadzipatula+ kwa anthu onse osakhala Aisiraeli.+ Atatero anaimirira ndi kuulula+ machimo awo+ ndi zolakwa za makolo awo.+
3 Pakuti pali anthu achilendo amene andiukira,Ndipo pali olamulira ankhanza amene akufuna moyo wanga.+Sanaike Mulungu patsogolo pawo.+ [Seʹlah.]