Salimo 35:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwo akadwala ndinali kuvala chiguduli,+Ndinali kusautsa moyo wanga mwa kusala kudya.+Ndipo mapemphero anga anali kubwerera kwa ine osayankhidwa.+ Salimo 109:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mawondo anga akugwedezeka chifukwa chosala kudya,+Ndawonda ndipo ndilibe mafuta alionse odzola.+
13 Iwo akadwala ndinali kuvala chiguduli,+Ndinali kusautsa moyo wanga mwa kusala kudya.+Ndipo mapemphero anga anali kubwerera kwa ine osayankhidwa.+