Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 17:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Poyankha Davide anauza Mfilisitiyo kuti: “Iwe ukubwera kwa ine ndi lupanga, mkondo ndi nthungo,+ koma ine ndikubwera kwa iwe m’dzina la Yehova wa makamu,+ Mulungu wa asilikali a Isiraeli, amene iweyo wam’tonza.+

  • Yeremiya 17:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Wodala ndi munthu aliyense amene amakhulupirira Yehova, amene amadalira Yehova.+

  • Luka 2:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Ndipo mwanayo anali kukulirakulira ndi kukhala wamphamvu.+ Nzeru zake zinali kuchuluka ndipo Mulungu anapitiriza kukondwera naye.+

  • 2 Timoteyo 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kuyambira pamene unali wakhanda,+ wadziwa malemba oyera amene angathe kukupatsa nzeru zokuthandiza kuti udzapulumuke+ kudzera m’chikhulupiriro chokhudza Khristu Yesu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena