1 Mafumu 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Baalati,+ ndi Tamara m’chipululu cha m’dzikolo. Salimo 74:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu munaphwanya mitu ya Leviyatani*+ kukhala zidutswazidutswa.Munaipereka kwa anthu monga chakudya, munaipereka kwa anthu okhala m’madera opanda madzi.+
14 Inu munaphwanya mitu ya Leviyatani*+ kukhala zidutswazidutswa.Munaipereka kwa anthu monga chakudya, munaipereka kwa anthu okhala m’madera opanda madzi.+