Ekisodo 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Choncho pa tsiku limenelo Yehova anapulumutsa Isiraeli m’manja mwa Aiguputo,+ ndipo Isiraeli anaona Aiguputo atafa m’mphepete mwa nyanja.+ Numeri 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chongofunika n’chakuti musam’pandukire Yehova.+ Komanso anthu a m’dzikolo musawaope,+ chifukwa ali ngati chakudya kwa ife. Alibenso chitetezo,+ koma ifeyo Yehova ali nafe.+ Musawaope ayi.”+
30 Choncho pa tsiku limenelo Yehova anapulumutsa Isiraeli m’manja mwa Aiguputo,+ ndipo Isiraeli anaona Aiguputo atafa m’mphepete mwa nyanja.+
9 Chongofunika n’chakuti musam’pandukire Yehova.+ Komanso anthu a m’dzikolo musawaope,+ chifukwa ali ngati chakudya kwa ife. Alibenso chitetezo,+ koma ifeyo Yehova ali nafe.+ Musawaope ayi.”+