Salimo 37:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Usapse mtima chifukwa cha anthu ochita zoipa.+Usakhumbe kukhala ngati anthu ochita zosalungama.+ Salimo 73:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti ndinachitira nsanje anthu odzitukumula,+Ndikamaona mtendere wa anthu oipa.+