Mateyu 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti kudzafika onamizira kukhala Khristu+ ndi aneneri onyenga,+ ndipo adzachita zizindikiro zamphamvu+ ndiponso zodabwitsa, kuti ngati n’kotheka, adzasocheretse ngakhale osankhidwawo.+ Maliko 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti kudzafika onamizira kukhala Khristu ndiponso aneneri onyenga,+ ndipo adzachita zizindikiro ndi zodabwitsa+ kuti ngati n’kotheka, adzasocheretse osankhidwawo.+
24 Pakuti kudzafika onamizira kukhala Khristu+ ndi aneneri onyenga,+ ndipo adzachita zizindikiro zamphamvu+ ndiponso zodabwitsa, kuti ngati n’kotheka, adzasocheretse ngakhale osankhidwawo.+
22 Pakuti kudzafika onamizira kukhala Khristu ndiponso aneneri onyenga,+ ndipo adzachita zizindikiro ndi zodabwitsa+ kuti ngati n’kotheka, adzasocheretse osankhidwawo.+