Deuteronomo 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Mneneri+ kapena wolota maloto+ akauka pakati panu n’kukupatsani chizindikiro kapena chodabwitsa cholosera zam’tsogolo,+ Deuteronomo 18:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mneneri akalankhula m’dzina la Yehova, koma mawuwo sanachitike kapena kukwaniritsidwa, ndiye kuti si Yehova amene walankhula mawu amenewo.+ Mneneriyo walankhula mawu amenewo mwa iye yekha, modzikuza. Iwe usachite naye mantha.’+ Mateyu 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Chenjerani ndi aneneri onyenga+ amene amabwera kwa inu atavala ngati nkhosa,+ koma mkati mwawo ali mimbulu yolusa.+
13 “Mneneri+ kapena wolota maloto+ akauka pakati panu n’kukupatsani chizindikiro kapena chodabwitsa cholosera zam’tsogolo,+
22 Mneneri akalankhula m’dzina la Yehova, koma mawuwo sanachitike kapena kukwaniritsidwa, ndiye kuti si Yehova amene walankhula mawu amenewo.+ Mneneriyo walankhula mawu amenewo mwa iye yekha, modzikuza. Iwe usachite naye mantha.’+
15 “Chenjerani ndi aneneri onyenga+ amene amabwera kwa inu atavala ngati nkhosa,+ koma mkati mwawo ali mimbulu yolusa.+