Yesaya 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munthu wochokera kufumbi adzawerama. Iye adzatsika, ndipo ngakhale maso a anthu okwezeka adzatsika.+ Yeremiya 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Uza mfumu ndi mayi a mfumu+ kuti, ‘Khalani pamalo apansi,+ pakuti chisoti chanu chaulemerero chidzachotsedwa pamutu panu ndi kuikidwa pansi.’+
15 Munthu wochokera kufumbi adzawerama. Iye adzatsika, ndipo ngakhale maso a anthu okwezeka adzatsika.+
18 “Uza mfumu ndi mayi a mfumu+ kuti, ‘Khalani pamalo apansi,+ pakuti chisoti chanu chaulemerero chidzachotsedwa pamutu panu ndi kuikidwa pansi.’+