Salimo 40:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wodala ndi munthu wamphamvu amene amakhulupirira Yehova,+Munthu amene sanacheukire anthu otsutsa,Kapena anthu amene anapatukira m’njira za mabodza.+ Yeremiya 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wodala ndi munthu aliyense amene amakhulupirira Yehova, amene amadalira Yehova.+
4 Wodala ndi munthu wamphamvu amene amakhulupirira Yehova,+Munthu amene sanacheukire anthu otsutsa,Kapena anthu amene anapatukira m’njira za mabodza.+