Deuteronomo 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Koma khalani tcheru ndipo musamale moyo wanu,+ kuti musaiwale zinthu zimene maso anu anaona,+ ndi kuti mitima yanu isaiwale zinthu zimenezo masiku onse a moyo wanu.+ Ana anu ndi zidzukulu zanu muziwauza za zinthu zimenezo,+ Salimo 103:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tamanda Yehova, iwe moyo wanga,Ndipo usaiwale zochita zake zonse.+
9 “Koma khalani tcheru ndipo musamale moyo wanu,+ kuti musaiwale zinthu zimene maso anu anaona,+ ndi kuti mitima yanu isaiwale zinthu zimenezo masiku onse a moyo wanu.+ Ana anu ndi zidzukulu zanu muziwauza za zinthu zimenezo,+