Ekisodo 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yehova anachitadi zimenezo, moti tizilombo touluka toyamwa magazi tinali ponseponse m’nyumba ya Farao, m’nyumba za atumiki ake ndi m’dziko lonse la Iguputo.+ Dziko linaipa chifukwa cha tizilombo timeneto.+ Salimo 105:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Analamula kuti pagwe tizilombo touluka toyamwa magazi,+Komanso ntchentche zoluma m’madera awo onse.+
24 Yehova anachitadi zimenezo, moti tizilombo touluka toyamwa magazi tinali ponseponse m’nyumba ya Farao, m’nyumba za atumiki ake ndi m’dziko lonse la Iguputo.+ Dziko linaipa chifukwa cha tizilombo timeneto.+
31 Analamula kuti pagwe tizilombo touluka toyamwa magazi,+Komanso ntchentche zoluma m’madera awo onse.+