Salimo 85:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tisonkhanitseni ndi kutibwezeretsa mwakale, inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Ndipo tichotsereni mkwiyo wanu.+ Maliro 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Inu Yehova, tibwezeni+ kwa inu ndipo ife tibwerera mwamsanga. Mubwezeretse zinthu zonse kuti zikhale ngati mmene zinalili kale.+
4 Tisonkhanitseni ndi kutibwezeretsa mwakale, inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Ndipo tichotsereni mkwiyo wanu.+
21 Inu Yehova, tibwezeni+ kwa inu ndipo ife tibwerera mwamsanga. Mubwezeretse zinthu zonse kuti zikhale ngati mmene zinalili kale.+