Yesaya 63:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 N’chifukwa chiyani inu Yehova mukutichititsa kuchoka panjira zanu? N’chifukwa chiyani mukuumitsa mtima wathu kuti tisakuopeni?+ Bwererani chifukwa cha atumiki anu, mafuko a cholowa chanu.+ Malaki 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kuyambira m’masiku a makolo anu mwakhala mukupatuka pa malamulo anga ndipo simunawasunge.+ Bwererani kwa ine ndipo ine ndibwerera kwa inu,”+ watero Yehova wa makamu. Koma inu mukunena kuti: “Tibwerere motani?”
17 N’chifukwa chiyani inu Yehova mukutichititsa kuchoka panjira zanu? N’chifukwa chiyani mukuumitsa mtima wathu kuti tisakuopeni?+ Bwererani chifukwa cha atumiki anu, mafuko a cholowa chanu.+
7 Kuyambira m’masiku a makolo anu mwakhala mukupatuka pa malamulo anga ndipo simunawasunge.+ Bwererani kwa ine ndipo ine ndibwerera kwa inu,”+ watero Yehova wa makamu. Koma inu mukunena kuti: “Tibwerere motani?”