Salimo 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndiye mphamvu kwa anthu ake,+Iye ndi malo achitetezo odzetsa chipulumutso chachikulu kwa wodzozedwa wake.+ Afilipi 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa zinthu zonse, ndimapeza mphamvu kuchokera kwa iye amene amandipatsa mphamvu.+
8 Yehova ndiye mphamvu kwa anthu ake,+Iye ndi malo achitetezo odzetsa chipulumutso chachikulu kwa wodzozedwa wake.+