Salimo 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Muimbireni nyimbo yatsopano.+Muimbireni choimbira cha zingwe ndi mtima wonse ndi kufuula mosangalala.+ Mateyu 22:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 ‘Ine ndine Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo’?+ Iye ndi Mulungu wa anthu amoyo, osati akufa.”+
3 Muimbireni nyimbo yatsopano.+Muimbireni choimbira cha zingwe ndi mtima wonse ndi kufuula mosangalala.+
32 ‘Ine ndine Mulungu wa Abulahamu, Mulungu wa Isaki ndi Mulungu wa Yakobo’?+ Iye ndi Mulungu wa anthu amoyo, osati akufa.”+