Salimo 146:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Wodala ndi munthu amene thandizo lake limachokera kwa Mulungu wa Yakobo,+Amene chiyembekezo chake chili mwa Yehova Mulungu wake,+ Yeremiya 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wodala ndi munthu aliyense amene amakhulupirira Yehova, amene amadalira Yehova.+
5 Wodala ndi munthu amene thandizo lake limachokera kwa Mulungu wa Yakobo,+Amene chiyembekezo chake chili mwa Yehova Mulungu wake,+ Yeremiya 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wodala ndi munthu aliyense amene amakhulupirira Yehova, amene amadalira Yehova.+