Salimo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wosautsikayu anaitana ndipo Yehova anamva.+Anamupulumutsa m’masautso ake onse.+ Yesaya 66:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Zinthu zonsezi ndinazipanga ndi dzanja langa, choncho zinakhalapo,”+ akutero Yehova. “Ine ndidzayang’ana munthu amene ali wosautsidwa, wosweka mtima,+ ndiponso wonjenjemera ndi mawu anga.+
2 “Zinthu zonsezi ndinazipanga ndi dzanja langa, choncho zinakhalapo,”+ akutero Yehova. “Ine ndidzayang’ana munthu amene ali wosautsidwa, wosweka mtima,+ ndiponso wonjenjemera ndi mawu anga.+