1 Samueli 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+ Salimo 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho dziwani kuti Yehova adzapatula wokhulupirika wake.+Yehova adzamva ndikaitana.+ Salimo 37:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pakuti Yehova amakonda chilungamo,+Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [ʽAʹyin]Adzawateteza mpaka kalekale.+Koma ana a anthu oipa adzaphedwa.+
9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+
28 Pakuti Yehova amakonda chilungamo,+Ndipo sadzasiya anthu ake okhulupirika.+ ע [ʽAʹyin]Adzawateteza mpaka kalekale.+Koma ana a anthu oipa adzaphedwa.+