Yobu 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa cha kuzunzika, diso langa layamba kuchita mdima.+Ziwalo zanga zonse zakhala ngati mthunzi. Salimo 38:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mtima wanga ukugunda kwambiri, ndipo mphamvu zanga zatha,Maso anga achita mdima.+ Salimo 42:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Misozi yanga yasanduka chakudya changa usana ndi usiku,+Pamene anthu akundifunsa tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+ Maliro 3:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Maso anga akungotuluka misozi mosalekeza,+
7 Chifukwa cha kuzunzika, diso langa layamba kuchita mdima.+Ziwalo zanga zonse zakhala ngati mthunzi.
3 Misozi yanga yasanduka chakudya changa usana ndi usiku,+Pamene anthu akundifunsa tsiku lonse kuti: “Mulungu wako ali kuti?”+