Salimo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Maso anga achita mdima chifukwa cha chisoni changa.+Maso anga akalamba chifukwa cha anthu onse ondichitira zoipa.+ Salimo 88:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Diso langa lafooka chifukwa cha kusautsika kwanga.+Ndaitana inu Yehova tsiku lonse.+Ndapemphera kwa inu nditakweza manja anga.+
7 Maso anga achita mdima chifukwa cha chisoni changa.+Maso anga akalamba chifukwa cha anthu onse ondichitira zoipa.+
9 Diso langa lafooka chifukwa cha kusautsika kwanga.+Ndaitana inu Yehova tsiku lonse.+Ndapemphera kwa inu nditakweza manja anga.+