Salimo 88:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Diso langa lachita mdima chifukwa cha kuvutika kwanga.+ Ndimaitana inu Yehova tsiku lonse.+Ndimapemphera kwa inu nditakweza manja anga.
9 Diso langa lachita mdima chifukwa cha kuvutika kwanga.+ Ndimaitana inu Yehova tsiku lonse.+Ndimapemphera kwa inu nditakweza manja anga.