Salimo 55:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Usiku, m’mawa ndi masana ndimakhala ndi nkhawa ndipo ndimakhala ndikulira,+Choncho Mulungu amamva mawu anga.+ Salimo 86:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndikomereni mtima inu Yehova,+Pakuti ndimaitana inu tsiku lonse.+
17 Usiku, m’mawa ndi masana ndimakhala ndi nkhawa ndipo ndimakhala ndikulira,+Choncho Mulungu amamva mawu anga.+