Salimo 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyendetseni m’choonadi chanu ndi kundiphunzitsa,+Pakuti inu ndinu Mulungu wa chipulumutso changa.+ ו [Waw]Chiyembekezo changa chili mwa inu tsiku lonse.+ Salimo 88:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Diso langa lafooka chifukwa cha kusautsika kwanga.+Ndaitana inu Yehova tsiku lonse.+Ndapemphera kwa inu nditakweza manja anga.+
5 Ndiyendetseni m’choonadi chanu ndi kundiphunzitsa,+Pakuti inu ndinu Mulungu wa chipulumutso changa.+ ו [Waw]Chiyembekezo changa chili mwa inu tsiku lonse.+
9 Diso langa lafooka chifukwa cha kusautsika kwanga.+Ndaitana inu Yehova tsiku lonse.+Ndapemphera kwa inu nditakweza manja anga.+