Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 8:54
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 54 Tsopano Solomo atangomaliza kupemphera kwa Yehova pemphero lonseli, ndi pempho lopempha chifundo, anaimirira patsogolo pa guwa lansembe la Yehova popeza nthawi yonseyi anali chogwada,+ manja ake atawatambasulira kumwamba.+

  • 2 Mbiri 6:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 (Pakuti Solomo anapanga nsanja+ yamkuwa n’kuiika pakati pa bwalo lamkati.+ Nsanjayo inali yaikulu mikono isanu m’litali, mikono isanu m’lifupi, ndipo kuchokera pansi kufika pamwamba inali yaitali mikono itatu. Iye anaimirira pansanjayo.) Atatero anagwada+ patsogolo pa mpingo wonse wa Isiraeli. Kenako anatambasula manja ake n’kuwakweza kumwamba.+

  • Salimo 143:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ine ndikupemphera nditakweza manja anga kwa inu.+

      Moyo wanga uli ngati dziko louma limene likulakalaka kuti muthetse ludzu lake.+ [Seʹlah.]

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena