Genesis 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Mulungu anati: “Madzi apansi pa thambo asonkhane malo amodzi, mtundanso uonekere.”+ Ndipo zinaterodi. Miyambo 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 iye asanapange dziko lapansi,+ zigwa zopanda kanthu, ndi zibuma zoyamba za dothi lachonde la padziko lapansi.+
9 Kenako Mulungu anati: “Madzi apansi pa thambo asonkhane malo amodzi, mtundanso uonekere.”+ Ndipo zinaterodi.
26 iye asanapange dziko lapansi,+ zigwa zopanda kanthu, ndi zibuma zoyamba za dothi lachonde la padziko lapansi.+