Yobu 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndangotsala mafupa okhaokha,+Ndipo pang’onong’ono n’kanafa.* Miyambo 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mtima wosangalala ndiwo mankhwala ochiritsa,+ koma mtima wosweka umaumitsa mafupa.+ Maliro 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano ayamba kuoneka akuda kuposa makala. Anthu sakuwazindikiranso mumsewu.+Khungu lawo lafota moti lamamatira kumafupa awo.+ Langoti gwaa ngati mtengo.
8 Tsopano ayamba kuoneka akuda kuposa makala. Anthu sakuwazindikiranso mumsewu.+Khungu lawo lafota moti lamamatira kumafupa awo.+ Langoti gwaa ngati mtengo.