Salimo 138:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mafumu onse a padziko lapansi adzakutamandani, inu Yehova,+Pakuti adzakhala atamva mawu a pakamwa panu. Yesaya 60:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mitundu ya anthu idzatsata kuwala kwako,+ ndipo mafumu+ adzatsata kunyezimira kwako.+ Zekariya 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu ambiri a mitundu ina ndiponso mitundu yamphamvu ya anthu idzabweradi kudzafunafuna Yehova wa makamu mu Yerusalemu.+ Idzabwera kudzakhazika pansi mtima wa Yehova.’
4 Mafumu onse a padziko lapansi adzakutamandani, inu Yehova,+Pakuti adzakhala atamva mawu a pakamwa panu.
22 Anthu ambiri a mitundu ina ndiponso mitundu yamphamvu ya anthu idzabweradi kudzafunafuna Yehova wa makamu mu Yerusalemu.+ Idzabwera kudzakhazika pansi mtima wa Yehova.’