Salimo 147:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amauza Yakobo mawu ake,+Ndipo amauza Isiraeli malangizo+ ake ndi zigamulo zake.+