Salimo 147:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye amapatsa zilombo chakudya chawo,+Amapatsanso ana a makwangwala chakudya chimene amalirira.+ Yoweli 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chifukwa chakuti mitsinje ya madzi yauma,+ ndipo moto wawononga malo odyetserako ziweto m’chipululu, zilombo zakutchire nazonso zikukufunani kwambiri.”+
20 Chifukwa chakuti mitsinje ya madzi yauma,+ ndipo moto wawononga malo odyetserako ziweto m’chipululu, zilombo zakutchire nazonso zikukufunani kwambiri.”+