Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 20:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako, Mose ndi Aroni anasonkhanitsa mpingo wonse pamodzi patsogolo pa thanthwelo, ndipo Mose anawauza kuti: “Tsopano tamverani anthu opanduka inu!+ Kodi tichite kukutulutsirani madzi m’thanthweli?”+

  • Yobu 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma Yobu anamuyankha kuti: “Ukulankhula ngati mmene amalankhulira akazi opusa.+ Kodi tizingolandira zabwino zokha kuchokera kwa Mulungu woona osalandiranso zoipa?”+ M’zonsezi Yobu sanachimwe ndi milomo yake.+

  • Salimo 141:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Inu Yehova, ikani mlonda pakamwa panga.+

      Ikani wolondera patsogolo pa milomo yanga.+

  • Miyambo 16:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Munthu wosakwiya msanga ndi wabwino kuposa munthu wamphamvu,+ ndipo munthu wolamulira mtima wake amaposa munthu wogonjetsa mzinda.+

  • Yakobo 3:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Paja tonsefe timapunthwa nthawi zambiri.+ Ngati wina sapunthwa pa mawu,+ ameneyo ndi munthu wangwiro,+ ndipo akhoza kulamuliranso thupi lake lonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena