Ekisodo 23:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Asakhale m’dziko lako, kuti asakuchimwitse pamaso panga. Ukatumikira milungu yawo, umenewo udzakhala msampha kwa iwe.”+ Oweruza 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho nanenso ndikuti, ‘Sindiwapitikitsa pamaso panu, koma akhala msampha kwa inu,+ ndipo milungu yawo ikhala ngati nyambo.’”+
33 Asakhale m’dziko lako, kuti asakuchimwitse pamaso panga. Ukatumikira milungu yawo, umenewo udzakhala msampha kwa iwe.”+
3 Choncho nanenso ndikuti, ‘Sindiwapitikitsa pamaso panu, koma akhala msampha kwa inu,+ ndipo milungu yawo ikhala ngati nyambo.’”+