1 Samueli 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musalankhule modzikweza kwambiri anthu inu,Pakamwa panu pasatuluke mawu odzikuza,+Pakuti Yehova ndi Mulungu wodziwa zonse.+Ndipo zochita za anthu, iye amaziyeza molondola.+ Salimo 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Milomo yachinyengo isowe chonena,+Milomo imene ikulankhula motsutsana ndi wolungama,+ yosadziletsa pa kudzikweza ndi kunyoza ena.+ Salimo 73:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kudzikweza kwawo kwafika kumwamba,+Akuyendayenda padziko lapansi ndipo lilime lawo likunena zilizonse zimene akufuna.+
3 Musalankhule modzikweza kwambiri anthu inu,Pakamwa panu pasatuluke mawu odzikuza,+Pakuti Yehova ndi Mulungu wodziwa zonse.+Ndipo zochita za anthu, iye amaziyeza molondola.+
18 Milomo yachinyengo isowe chonena,+Milomo imene ikulankhula motsutsana ndi wolungama,+ yosadziletsa pa kudzikweza ndi kunyoza ena.+
9 Kudzikweza kwawo kwafika kumwamba,+Akuyendayenda padziko lapansi ndipo lilime lawo likunena zilizonse zimene akufuna.+