Salimo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yamikani Yehova poimba zeze.+Muimbireni nyimbo zomutamanda ndi choimbira cha zingwe 10.+ Salimo 81:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yambani kuimba nyimbo+ ndipo tengani maseche,+Zeze womveka mosangalatsa pamodzi ndi choimbira cha zingwe.+ Salimo 149:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atamande dzina lake mwa kuvina.+Amuimbire nyimbo zomutamanda ndi maseche ndi zeze,+
2 Yambani kuimba nyimbo+ ndipo tengani maseche,+Zeze womveka mosangalatsa pamodzi ndi choimbira cha zingwe.+