Salimo 57:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iwe mtima wanga, galamuka.+Iwe choimbira cha zingwe, galamuka, ndi iwenso zeze.+Ndidzadzuka m’bandakucha usanafike.
8 Iwe mtima wanga, galamuka.+Iwe choimbira cha zingwe, galamuka, ndi iwenso zeze.+Ndidzadzuka m’bandakucha usanafike.