Salimo 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Moyo wake udzasangalala ndi ubwino wa Mulungu,+Mbadwa zake zidzatenga dziko lapansi kukhala lawo.+ Salimo 37:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tsiku lililonse amakomera mtima ena ndi kuwakongoza zinthu,+Ndipo ana ake adzalandira madalitso.+ Salimo 102:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ana a atumiki anu adzapitiriza kukhala motetezeka pamaso panu.+Ndipo ana awo adzakhazikika pamaso panu.”+ Machitidwe 2:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Pakuti lonjezoli+ laperekedwa kwa inu, kwa ana anu ndi kwa onse akutali,+ onse amene Yehova Mulungu wathu angawasankhe.”+
13 Moyo wake udzasangalala ndi ubwino wa Mulungu,+Mbadwa zake zidzatenga dziko lapansi kukhala lawo.+
28 Ana a atumiki anu adzapitiriza kukhala motetezeka pamaso panu.+Ndipo ana awo adzakhazikika pamaso panu.”+
39 Pakuti lonjezoli+ laperekedwa kwa inu, kwa ana anu ndi kwa onse akutali,+ onse amene Yehova Mulungu wathu angawasankhe.”+