Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+ Luka 1:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 za kutipulumutsa kwa adani athu ndiponso m’manja mwa onse odana nafe.+