Nehemiya 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mulungu wanga, mundikumbukire+ pa zabwino+ zonse zimene ndachitira anthu awa.+ Miyambo 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+
7 Anthu akamakumbukira zabwino zimene munthu wolungama anali kuchita, amam’dalitsa,+ koma dzina la anthu oipa lidzawola.+