Genesis 41:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Farao anauzanso Yosefe kuti: “Tsopano ndikukuika kukhala woyang’anira dziko lonse la Iguputo.”+ Yobu 36:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sadzachotsa maso ake pa aliyense wolungama.+Adzaika mafumu pamipando yachifumu,+Adzawachititsa kuti alamulire kwamuyaya, ndipo iwo adzakhala ndi mphamvu zambiri.
7 Sadzachotsa maso ake pa aliyense wolungama.+Adzaika mafumu pamipando yachifumu,+Adzawachititsa kuti alamulire kwamuyaya, ndipo iwo adzakhala ndi mphamvu zambiri.