Genesis 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo iye anakhulupirira mwa Yehova,+ ndipo Mulunguyo anamuona Abulamu ngati wolungama.+ 2 Akorinto 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano, popeza tili ndi mtima wachikhulupiriro wofanana ndi umene anaunena kuti: “Ndinali ndi chikhulupiriro, chotero ndinalankhula,”+ ifenso tili ndi chikhulupiriro, chotero tikulankhula, Aheberi 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chikhulupiriro+ ndicho chiyembekezo chotsimikizika cha zinthu zoyembekezeredwa,+ umboni wooneka wa zinthu zenizeni, ngakhale kuti n’zosaoneka.+
13 Tsopano, popeza tili ndi mtima wachikhulupiriro wofanana ndi umene anaunena kuti: “Ndinali ndi chikhulupiriro, chotero ndinalankhula,”+ ifenso tili ndi chikhulupiriro, chotero tikulankhula,
11 Chikhulupiriro+ ndicho chiyembekezo chotsimikizika cha zinthu zoyembekezeredwa,+ umboni wooneka wa zinthu zenizeni, ngakhale kuti n’zosaoneka.+