Salimo 136:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yamikani Mulungu wa milungu:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+