Salimo 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Inu oopa Yehova, m’tamandeni!+Inu nonse mbewu ya Yakobo, m’patseni ulemerero!+Ndipo muopeni, inu nonse mbewu ya Isiraeli.+ Chivumbulutso 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komanso, kunamveka mawu ochokera kumpando wachifumu akuti: “Muzitamanda Mulungu wathu, inu nonse akapolo+ ake, inu omuopa, olemekezeka ndi onyozeka omwe.”+
23 Inu oopa Yehova, m’tamandeni!+Inu nonse mbewu ya Yakobo, m’patseni ulemerero!+Ndipo muopeni, inu nonse mbewu ya Isiraeli.+
5 Komanso, kunamveka mawu ochokera kumpando wachifumu akuti: “Muzitamanda Mulungu wathu, inu nonse akapolo+ ake, inu omuopa, olemekezeka ndi onyozeka omwe.”+