Salimo 119:111 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 111 Ndatenga zikumbutso zanu kukhala chuma changa mpaka kalekale,+Pakuti zimakondweretsa mtima wanga.+ Yeremiya 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mawu anu anandipeza ndipo ndinawadya.+ Mawu anu amandikondweretsa+ ndi kusangalatsa mtima wanga,+ pakuti ine ndimatchedwa ndi dzina lanu,+ inu Yehova Mulungu wa makamu.+
111 Ndatenga zikumbutso zanu kukhala chuma changa mpaka kalekale,+Pakuti zimakondweretsa mtima wanga.+
16 Mawu anu anandipeza ndipo ndinawadya.+ Mawu anu amandikondweretsa+ ndi kusangalatsa mtima wanga,+ pakuti ine ndimatchedwa ndi dzina lanu,+ inu Yehova Mulungu wa makamu.+